Levitiko 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ngati munthu akupereka nsembe yamgwirizano+ kwa Yehova kuti akwaniritse lonjezo lake kapena kuti ikhale nsembe yaufulu, azipereka ngʼombe kapena nkhosa yopanda chilema, kuti Mulungu ailandire. Izikhala yopanda chilema chilichonse.
21 Ngati munthu akupereka nsembe yamgwirizano+ kwa Yehova kuti akwaniritse lonjezo lake kapena kuti ikhale nsembe yaufulu, azipereka ngʼombe kapena nkhosa yopanda chilema, kuti Mulungu ailandire. Izikhala yopanda chilema chilichonse.