Levitiko 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “‘Ngati munthu akupereka nsembe yambewu+ kwa Yehova, azipereka ufa wosalala. Azithira mafuta nʼkuika lubani* pa ufawo.+ Levitiko 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano lamulo la nsembe yambewu+ ndi ili: Ana a Aroni azibweretsa nsembeyi pamaso pa Yehova patsogolo pa guwa lansembe.
2 “‘Ngati munthu akupereka nsembe yambewu+ kwa Yehova, azipereka ufa wosalala. Azithira mafuta nʼkuika lubani* pa ufawo.+
14 Tsopano lamulo la nsembe yambewu+ ndi ili: Ana a Aroni azibweretsa nsembeyi pamaso pa Yehova patsogolo pa guwa lansembe.