Ekisodo 29:31, 32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako udzatenge nkhosa yowaikira kuti akhale ansembe nʼkuwiritsa nyama yake mʼmalo oyera.+ 32 Aroni ndi ana ake adye+ nyama ya nkhosayo ndi mkate umene uli mʼdengu, adyere pakhomo la chihema chokumanako. 1 Akorinto 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi simukudziwa kuti anthu amene amagwira ntchito zopatulika amadya zamʼkachisi, ndipo amene amatumikira kuguwa lansembe nthawi zonse amalandira zina mwa zinthu zoperekedwa paguwa lansembelo?+
31 Kenako udzatenge nkhosa yowaikira kuti akhale ansembe nʼkuwiritsa nyama yake mʼmalo oyera.+ 32 Aroni ndi ana ake adye+ nyama ya nkhosayo ndi mkate umene uli mʼdengu, adyere pakhomo la chihema chokumanako.
13 Kodi simukudziwa kuti anthu amene amagwira ntchito zopatulika amadya zamʼkachisi, ndipo amene amatumikira kuguwa lansembe nthawi zonse amalandira zina mwa zinthu zoperekedwa paguwa lansembelo?+