Ekisodo 29:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Udzatenga masiku 7 poperekera guwa lansembelo nsembe yophimba machimo. Udzaliyeretse kuti likhale guwa lansembe loyera koposa.+ Aliyense wogwira guwa lansembe azikhala woyera.
37 Udzatenga masiku 7 poperekera guwa lansembelo nsembe yophimba machimo. Udzaliyeretse kuti likhale guwa lansembe loyera koposa.+ Aliyense wogwira guwa lansembe azikhala woyera.