4 Nyama zimene mungathe kudya+ ndi izi: ngʼombe, nkhosa, mbuzi, 5 mbawala, insa, ngondo, mbuzi yakuthengo, mphalapala, nkhosa yakuthengo ndi nkhosa yamʼmapiri. 6 Mungathe kudya nyama iliyonse ya ziboda zogawanika, zokhala ndi mpata pakati, imenenso imabzikula.