-
Deuteronomo 14:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Koma musamadye nyama izi zokha zimene zimabzikula kapena zimene zili ndi ziboda zogawanika: ngamila, kalulu ndi mbira, chifukwa zimabzikula koma si zogawanika ziboda. Nyama zimenezi nʼzodetsedwa kwa inu.+ 8 Musamadyenso nkhumba chifukwa ndi ya ziboda zogawanika koma sibzikula. Imeneyi ndi yodetsedwa kwa inu. Musamadye nyama yake kapena kuikhudza ikafa.
-