Deuteronomo 14:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa zinthu zonse zokhala mʼmadzi, zimene mungadye ndi izi: Chilichonse chimene chili ndi zipsepse ndi mamba mungadye.+ 10 Koma musamadye chilichonse chimene chilibe zipsepse ndi mamba. Chimenecho nʼchodetsedwa kwa inu.
9 Pa zinthu zonse zokhala mʼmadzi, zimene mungadye ndi izi: Chilichonse chimene chili ndi zipsepse ndi mamba mungadye.+ 10 Koma musamadye chilichonse chimene chilibe zipsepse ndi mamba. Chimenecho nʼchodetsedwa kwa inu.