Yesaya 66:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu amene akudzipatula nʼkudziyeretsa potsatira fano limene lili pakati pa mundawo,*+ amene akudya nyama ya nkhumba,+ zinthu zonyansa komanso mbewa,+ onsewo adzathera limodzi,” akutero Yehova.
17 Anthu amene akudzipatula nʼkudziyeretsa potsatira fano limene lili pakati pa mundawo,*+ amene akudya nyama ya nkhumba,+ zinthu zonyansa komanso mbewa,+ onsewo adzathera limodzi,” akutero Yehova.