Levitiko 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma ngati chikangacho chikuoneka choyera ndipo sichinalowe mkati mwa khungu, komanso cheya sichinasanduke choyera, wansembe azimuika munthuyo kwayekha kwa masiku 7.+ Levitiko 13:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Wansembe aziona nthendayo, ndipo azisunga chinthucho kwachokha kwa masiku 7.+ Levitiko 14:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 wansembe azituluka mʼnyumbamo nʼkukaima pakhomo, ndipo azitseka nyumbayo masiku 7.+ Numeri 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Miriamu anatulutsidwa kukakhala kunja kwa msasa kwa masiku 7,+ ndipo anthuwo sanasamuke mpaka Miriamu atamubweretsanso mumsasa.
4 Koma ngati chikangacho chikuoneka choyera ndipo sichinalowe mkati mwa khungu, komanso cheya sichinasanduke choyera, wansembe azimuika munthuyo kwayekha kwa masiku 7.+
15 Choncho Miriamu anatulutsidwa kukakhala kunja kwa msasa kwa masiku 7,+ ndipo anthuwo sanasamuke mpaka Miriamu atamubweretsanso mumsasa.