Levitiko 23:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ili ndi sabata lopuma pa ntchito zanu zonse, ndipo muzisonyeza kuti mukudzimvera chisoni+ chifukwa cha machimo anu madzulo pa tsiku la 9 la mweziwo. Muzisunga sabata kuyambira madzulo mpaka madzulo tsiku lotsatira.”
32 Ili ndi sabata lopuma pa ntchito zanu zonse, ndipo muzisonyeza kuti mukudzimvera chisoni+ chifukwa cha machimo anu madzulo pa tsiku la 9 la mweziwo. Muzisunga sabata kuyambira madzulo mpaka madzulo tsiku lotsatira.”