Levitiko 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aziphimba machimo a malo oyera chifukwa cha zinthu zodetsa zimene Aisiraeli achita komanso chifukwa cha zolakwa ndi machimo awo.+ Azichita zimenezi ndi chihema chokumanako chimene chili pakati pa Aisiraeli, amene amachita zinthu zodetsa.
16 Aziphimba machimo a malo oyera chifukwa cha zinthu zodetsa zimene Aisiraeli achita komanso chifukwa cha zolakwa ndi machimo awo.+ Azichita zimenezi ndi chihema chokumanako chimene chili pakati pa Aisiraeli, amene amachita zinthu zodetsa.