14 Moyo wa nyama iliyonse ndi magazi ake chifukwa mʼmagazimo ndi mmene muli moyo. Nʼchifukwa chake ndauza Aisiraeli kuti: “Musamadye magazi a nyama iliyonse, chifukwa moyo wa nyama ina iliyonse ndi magazi ake. Aliyense wodya magaziwo ayenera kuphedwa.”+