Levitiko 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Usagone ndi mchemwali wa mayi ako kapena mchemwali wa bambo ako, chifukwa kuchita zimenezo nʼkuchititsa manyazi mʼbale wako.+ Iwo aziyankha mlandu wa kulakwa kwawo.
19 Usagone ndi mchemwali wa mayi ako kapena mchemwali wa bambo ako, chifukwa kuchita zimenezo nʼkuchititsa manyazi mʼbale wako.+ Iwo aziyankha mlandu wa kulakwa kwawo.