Levitiko 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Munthu akachimwa ndipo wachita mosakhulupirika kwa Yehova+ ponamiza mnzake pa chinthu chimene anamusungitsa,+ kapena chimene anamubwereka, kapena wamubera mnzake, kapena wamuchitira chinyengo, Miyambo 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova amanyansidwa ndi milomo yonama,+Koma anthu amene amachita zinthu mokhulupirika amamusangalatsa. Aefeso 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho, popeza tsopano mwataya chinyengo, aliyense wa inu azilankhula zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo zolumikizana.+
2 “Munthu akachimwa ndipo wachita mosakhulupirika kwa Yehova+ ponamiza mnzake pa chinthu chimene anamusungitsa,+ kapena chimene anamubwereka, kapena wamubera mnzake, kapena wamuchitira chinyengo,
22 Yehova amanyansidwa ndi milomo yonama,+Koma anthu amene amachita zinthu mokhulupirika amamusangalatsa.
25 Choncho, popeza tsopano mwataya chinyengo, aliyense wa inu azilankhula zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo zolumikizana.+