Levitiko 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngati akupereka ngʼombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza, azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako. Levitiko 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Isakhale yakhungu, yothyoka fupa, yotemeka, yokhala ndi njerewere, nkhanambo* kapena zipere. Musamapereke kwa Yehova nyama zoterezi kapena kuwotcha nyama zoterezi paguwa lansembe la Yehova.
3 Ngati akupereka ngʼombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza, azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako.
22 Isakhale yakhungu, yothyoka fupa, yotemeka, yokhala ndi njerewere, nkhanambo* kapena zipere. Musamapereke kwa Yehova nyama zoterezi kapena kuwotcha nyama zoterezi paguwa lansembe la Yehova.