Levitiko 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ngati akupereka mundawo Chaka cha Ufulu chitadutsa, wansembe azimuwerengera mtengo wake mogwirizana ndi zaka zimene zatsala kukafika mʼChaka cha Ufulu chotsatira, ndipo azichotsera pa mtengo wake womwe unaikidwa.+
18 Koma ngati akupereka mundawo Chaka cha Ufulu chitadutsa, wansembe azimuwerengera mtengo wake mogwirizana ndi zaka zimene zatsala kukafika mʼChaka cha Ufulu chotsatira, ndipo azichotsera pa mtengo wake womwe unaikidwa.+