Ezekieli 36:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pa nthawiyo mudzakumbukira njira zanu zoipa ndi zochita zanu zimene sizinali zabwino. Mudzadzimvera chisoni chifukwa cha machimo anu komanso zinthu zonyansa zimene munkachita.+
31 Pa nthawiyo mudzakumbukira njira zanu zoipa ndi zochita zanu zimene sizinali zabwino. Mudzadzimvera chisoni chifukwa cha machimo anu komanso zinthu zonyansa zimene munkachita.+