Levitiko 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Isakhale yakhungu, yothyoka fupa, yotemeka, yokhala ndi njerewere, nkhanambo* kapena zipere. Musamapereke kwa Yehova nyama zoterezi kapena kuwotcha nyama zoterezi paguwa lansembe la Yehova. Deuteronomo 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Musamapereke kwa Yehova Mulungu wanu nsembe ya ngʼombe kapena nkhosa imene ili ndi chilema kapena vuto lililonse, chifukwa idzakhala yonyansa kwa Yehova Mulungu wanu.+
22 Isakhale yakhungu, yothyoka fupa, yotemeka, yokhala ndi njerewere, nkhanambo* kapena zipere. Musamapereke kwa Yehova nyama zoterezi kapena kuwotcha nyama zoterezi paguwa lansembe la Yehova.
17 “Musamapereke kwa Yehova Mulungu wanu nsembe ya ngʼombe kapena nkhosa imene ili ndi chilema kapena vuto lililonse, chifukwa idzakhala yonyansa kwa Yehova Mulungu wanu.+