Levitiko 23:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kwa masiku 7 muzipereka nsembe yowotcha pamoto kwa Yehova. Pa tsiku la 8 muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzipereka nsembe yowotcha pamoto kwa Yehova. Umenewu ndi msonkhano wapadera. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa. Levitiko 23:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pa tsiku la 15 la mwezi wa 7, mukakolola zinthu zamʼmunda mwanu, muzichita chikondwerero cha Yehova masiku 7.+ Tsiku loyamba la chikondwererocho ndi tsiku lopuma pa ntchito zanu zonse, ndipo muzipumanso pa ntchito zanu zonse pa tsiku la 8.+
36 Kwa masiku 7 muzipereka nsembe yowotcha pamoto kwa Yehova. Pa tsiku la 8 muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzipereka nsembe yowotcha pamoto kwa Yehova. Umenewu ndi msonkhano wapadera. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa.
39 Pa tsiku la 15 la mwezi wa 7, mukakolola zinthu zamʼmunda mwanu, muzichita chikondwerero cha Yehova masiku 7.+ Tsiku loyamba la chikondwererocho ndi tsiku lopuma pa ntchito zanu zonse, ndipo muzipumanso pa ntchito zanu zonse pa tsiku la 8.+