-
Yoswa 13:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kenako Mose anagawira cholowa fuko la Rubeni motsatira mabanja awo.
-
-
Yoswa 13:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Komanso Mose anagawira cholowa fuko la Gadi motsatira mabanja awo.
-