Numeri 32:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ataroti, Diboni, Yazeri, Nimira, Hesiboni,+ Eleyale, Sebamu, Nebo+ komanso Beoni,+ 4 ndi madera amene Yehova anawagonjetsa kuti akhale a Aisiraeli.+ Madera amenewa ndi abwino kwa ziweto, ndipo atumiki anufe tili ndi ziweto zambiri.”+
3 “Ataroti, Diboni, Yazeri, Nimira, Hesiboni,+ Eleyale, Sebamu, Nebo+ komanso Beoni,+ 4 ndi madera amene Yehova anawagonjetsa kuti akhale a Aisiraeli.+ Madera amenewa ndi abwino kwa ziweto, ndipo atumiki anufe tili ndi ziweto zambiri.”+