-
Numeri 26:53, 54Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
53 “Anthu amenewa uwagawire dzikoli kuti likhale cholowa chawo, potengera mndandanda wa mayinawo.*+ 54 Amene ali ndi anthu ambiri apatsidwe dziko lalikulu monga cholowa chake, ndipo amene ali ndi anthu ochepa apatsidwe dziko lalingʼono monga cholowa chake.+ Aliyense apatsidwe cholowacho mogwirizana ndi chiwerengero cha anthu ake.
-