Levitiko 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Moto wapaguwa lansembe uziyaka nthawi zonse. Usamazime. Wansembe aziikapo nkhuni+ mʼmawa uliwonse nʼkuikapo nsembe yopsereza. Akatero aziwotcha mafuta a nsembe yamgwirizano pamotopo.+
12 Moto wapaguwa lansembe uziyaka nthawi zonse. Usamazime. Wansembe aziikapo nkhuni+ mʼmawa uliwonse nʼkuikapo nsembe yopsereza. Akatero aziwotcha mafuta a nsembe yamgwirizano pamotopo.+