Ekisodo 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Upangenso nsalu za ubweya wa mbuzi+ zoyala pachihemacho. Nsaluzo zikhale zokwana 11.+ Ekisodo 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Upangenso chophimba chihemacho cha zikopa za nkhosa zonyika mu utoto wofiira ndi chophimba chinanso pamwamba pake cha zikopa za akatumbu.+
14 Upangenso chophimba chihemacho cha zikopa za nkhosa zonyika mu utoto wofiira ndi chophimba chinanso pamwamba pake cha zikopa za akatumbu.+