Ekisodo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo ana aamuna a Merari anali Mali ndi Musi. Amenewa anali mabanja a Alevi mogwirizana ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+ Numeri 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mabanja a Amali ndi Amusi anachokera mwa Merari. Amenewa ndi amene anali mabanja a Amerari.+
19 Ndipo ana aamuna a Merari anali Mali ndi Musi. Amenewa anali mabanja a Alevi mogwirizana ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+