Numeri 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova kapena akachita lumbiro+ lodzimana, asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Azichita zonse zimene walonjezazo.+ Mlaliki 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa Mulungu sasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+
2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova kapena akachita lumbiro+ lodzimana, asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Azichita zonse zimene walonjezazo.+
4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa Mulungu sasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+