2 Samueli 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu amene ananyamula+ Likasa la Yehova atangoyenda mapazi 6, Davide anapereka nsembe ngʼombe yamphongo ndi chiweto chonenepa. 1 Mbiri 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Alevi anakanyamula Likasa la Mulungu woona pamapewa awo pogwiritsa ntchito ndodo,+ mogwirizana ndi zimene Mose anawalamula potsatira mawu a Yehova.
13 Anthu amene ananyamula+ Likasa la Yehova atangoyenda mapazi 6, Davide anapereka nsembe ngʼombe yamphongo ndi chiweto chonenepa.
15 Ndiyeno Alevi anakanyamula Likasa la Mulungu woona pamapewa awo pogwiritsa ntchito ndodo,+ mogwirizana ndi zimene Mose anawalamula potsatira mawu a Yehova.