Levitiko 27:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mtengo uliwonse womwe unaikidwa uzikhala wofanana ndi sekeli yakumalo oyera. Sekeli imodzi izikwana magera* 20.
25 Mtengo uliwonse womwe unaikidwa uzikhala wofanana ndi sekeli yakumalo oyera. Sekeli imodzi izikwana magera* 20.