Numeri 1:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ 5 Mayina a amuna amene akuthandizeni ndi awa: kuchokera ku fuko la Rubeni, Elizuri+ mwana wa Sedeuri,
4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ 5 Mayina a amuna amene akuthandizeni ndi awa: kuchokera ku fuko la Rubeni, Elizuri+ mwana wa Sedeuri,