Numeri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ Numeri 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa ana a Yosefe: kuchokera ku fuko la Efuraimu,+ Elisama mwana wa Amihudi, kuchokera ku fuko la Manase, Gamaliyeli mwana wa Pedazuri,
4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+
10 Pa ana a Yosefe: kuchokera ku fuko la Efuraimu,+ Elisama mwana wa Amihudi, kuchokera ku fuko la Manase, Gamaliyeli mwana wa Pedazuri,