-
Ekisodo 12:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 mudzawauze kuti, ‘Umenewu ndi mwambo wopereka nsembe ya Pasika kwa Yehova, amene anadumpha nyumba za Aisiraeli mu Iguputo pamene ankapha Aiguputo ndi mliri, koma anapulumutsa mabanja athu.’”
Atatero, anthuwo anagwada nʼkuweramira pansi.
-