Ekisodo 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Adzadye nyamayo usiku umenewu.+ Adzaiwotche pamoto ndipo adzaidye pamodzi ndi mikate yopanda zofufumitsa+ ndi masamba owawa.+
8 Adzadye nyamayo usiku umenewu.+ Adzaiwotche pamoto ndipo adzaidye pamodzi ndi mikate yopanda zofufumitsa+ ndi masamba owawa.+