-
2 Mbiri 30:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Atatero anapha nyama ya Pasika pa tsiku la 14 la mwezi wachiwiri. Ansembe ndi Alevi anachita manyazi moti anadziyeretsa nʼkubweretsa nsembe zopsereza kunyumba ya Yehova.
-