Numeri 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Posamutsa chihema chokumanako,+ gulu la Alevi lizikhala pakati pa magulu enawo. Dongosolo limene azitsatira posamuka,+ ndi limenenso azitsatira pomanga misasa yawo, aliyense pamalo ake, mogwirizana ndi gulu lawo la mafuko atatu. Numeri 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mabanja a Agerisoni ankamanga misasa yawo kumbuyo kwa chihema,+ mbali yakumadzulo. Numeri 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mabanja a ana a Kohati ankamanga msasa wawo kumʼmwera kwa chihema.+ Numeri 3:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mtsogoleri wa nyumba ya mabanja a Merari anali Zuriyeli, mwana wa Abihaili. Iwo ankamanga msasa wawo kumpoto kwa chihema.+ Numeri 3:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Amene ankamanga msasa wawo kumʼmawa kwa chihema, kumbali yotulukira dzuwa, anali Mose ndi Aroni, ndiponso ana a Aroni. Ntchito yawo inali kutumikira mʼmalo opatulika, mʼmalo mwa Aisiraeli. Munthu wamba aliyense* amene wayandikira malowo, ankayenera kuphedwa.+
17 Posamutsa chihema chokumanako,+ gulu la Alevi lizikhala pakati pa magulu enawo. Dongosolo limene azitsatira posamuka,+ ndi limenenso azitsatira pomanga misasa yawo, aliyense pamalo ake, mogwirizana ndi gulu lawo la mafuko atatu.
35 Mtsogoleri wa nyumba ya mabanja a Merari anali Zuriyeli, mwana wa Abihaili. Iwo ankamanga msasa wawo kumpoto kwa chihema.+
38 Amene ankamanga msasa wawo kumʼmawa kwa chihema, kumbali yotulukira dzuwa, anali Mose ndi Aroni, ndiponso ana a Aroni. Ntchito yawo inali kutumikira mʼmalo opatulika, mʼmalo mwa Aisiraeli. Munthu wamba aliyense* amene wayandikira malowo, ankayenera kuphedwa.+