Numeri 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Aisiraeli azikhoma matenti awo, pamalo amene gulu lawo la mafuko atatu+ lapatsidwa, munthu aliyense azikhala pafupi ndi chizindikiro cha nyumba ya makolo ake. Iwo azikhoma matenti awo mozungulira chihema chokumanako komanso moyangʼana chihemacho. Numeri 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Aisiraeli anachita zonse mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose. Dongosolo limene analitsatira pomanga misasa yawo mʼmagulu a mafuko atatu,+ ndi limenenso anatsatira posamuka,+ aliyense mʼbanja lake mogwirizana ndi nyumba ya makolo ake.
2 “Aisiraeli azikhoma matenti awo, pamalo amene gulu lawo la mafuko atatu+ lapatsidwa, munthu aliyense azikhala pafupi ndi chizindikiro cha nyumba ya makolo ake. Iwo azikhoma matenti awo mozungulira chihema chokumanako komanso moyangʼana chihemacho.
34 Aisiraeli anachita zonse mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose. Dongosolo limene analitsatira pomanga misasa yawo mʼmagulu a mafuko atatu,+ ndi limenenso anatsatira posamuka,+ aliyense mʼbanja lake mogwirizana ndi nyumba ya makolo ake.