Ekisodo 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho madzulo amenewo kunabwera zinziri zimene zinakuta msasa wonse,+ ndipo mʼmawa kunachita mame kuzungulira msasa wonsewo. Salimo 78:26, 27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anachititsa kuti mphepo yakumʼmawa iwombe mumlengalenga,Komanso ndi mphamvu zake, anachititsa kuti mphepo yakumʼmwera iwombe.+ 27 Iye anawagwetsera nyama yochuluka ngati fumbi,Anawagwetsera mbalame zochuluka ngati mchenga wamʼmbali mwa nyanja.
13 Choncho madzulo amenewo kunabwera zinziri zimene zinakuta msasa wonse,+ ndipo mʼmawa kunachita mame kuzungulira msasa wonsewo.
26 Anachititsa kuti mphepo yakumʼmawa iwombe mumlengalenga,Komanso ndi mphamvu zake, anachititsa kuti mphepo yakumʼmwera iwombe.+ 27 Iye anawagwetsera nyama yochuluka ngati fumbi,Anawagwetsera mbalame zochuluka ngati mchenga wamʼmbali mwa nyanja.