Ekisodo 33:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova ankalankhula ndi Mose pamasomʼpamaso,+ mmene munthu amalankhulira ndi munthu mnzake. Mose akabwerera kumsasa, mtumiki wake Yoswa,+ mwana wa Nuni, sankachoka kuchihemako. Deuteronomo 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma mu Isiraeli simunakhalenso mneneri aliyense wofanana ndi Mose,+ amene Yehova ankamudziwa bwino kwambiri.*+
11 Yehova ankalankhula ndi Mose pamasomʼpamaso,+ mmene munthu amalankhulira ndi munthu mnzake. Mose akabwerera kumsasa, mtumiki wake Yoswa,+ mwana wa Nuni, sankachoka kuchihemako.
10 Koma mu Isiraeli simunakhalenso mneneri aliyense wofanana ndi Mose,+ amene Yehova ankamudziwa bwino kwambiri.*+