-
Levitiko 1:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Uza Aisiraeli* kuti, ‘Ngati munthu aliyense akufuna kupereka chiweto kwa Yehova kuti ikhale nsembe, azipereka ngʼombe, nkhosa kapena mbuzi.+
3 Ngati akupereka ngʼombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza, azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako.
-