Levitiko 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka nsembe yamgwirizano*+ kwa Yehova ndipo akufuna kupereka ngʼombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema. Levitiko 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Azipereka mbali ina ya nsembe yamgwirizanoyo ngati nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova.+ Azipereka mafuta+ okuta matumbo ndi mafuta onse amene ali pamatumbo. Levitiko 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano lamulo la nsembe yamgwirizano+ imene aliyense azipereka kwa Yehova ndi ili:
3 “‘Ngati akupereka nsembe yamgwirizano*+ kwa Yehova ndipo akufuna kupereka ngʼombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema.
3 Azipereka mbali ina ya nsembe yamgwirizanoyo ngati nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova.+ Azipereka mafuta+ okuta matumbo ndi mafuta onse amene ali pamatumbo.