27 Ngati munthu aliyense pakati panu wachimwa mosazindikira pochita chimodzi mwa zinthu zimene Yehova analamula kuti asachite+ ndipo wapalamula, 28 kapena ngati wadziwa kuti wachimwa, azibweretsa mbuzi yaingʼono yaikazi, yopanda chilema kuti ikhale nsembe chifukwa cha tchimo lakelo.