Numeri 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Yehova anatsika mʼchipilala chamtambo+ nʼkuima pakhomo la chihema chokumanako. Kenako anaitana Aroni ndi Miriamu ndipo onse anapita. Numeri 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma gulu lonselo linayamba kunena zoti liwaponye miyala.+ Kenako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa Aisiraeli onse+ pamwamba pa chihema chokumanako.
5 Ndiyeno Yehova anatsika mʼchipilala chamtambo+ nʼkuima pakhomo la chihema chokumanako. Kenako anaitana Aroni ndi Miriamu ndipo onse anapita.
10 Koma gulu lonselo linayamba kunena zoti liwaponye miyala.+ Kenako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa Aisiraeli onse+ pamwamba pa chihema chokumanako.