-
Numeri 7:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Yehova anauza Mose kuti: “Mtsogoleri mmodzi patsiku, kwa masiku otsatizana, azipereka zopereka zake kuti zigwiritsidwe ntchito potsegulira guwa lansembe.”
-