-
Numeri 16:21, 22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 “Chokani pakati pa gululi, kuti ndiwawononge kamodzinʼkamodzi.”+ 22 Anthuwo atamva zimenezi anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi, nʼkunena kuti: “Chonde Mulungu, inu Mulungu amene amapereka moyo kwa anthu onse,*+ kodi mukupsera mtima gulu lonseli+ chifukwa cha kuchimwa kwa munthu mmodzi yekha?”
-