Numeri 1:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Alevi azimanga matenti awo mozungulira chihema cha Umboni kuti mkwiyo wa Mulungu usayakire Aisiraeli.+ Aleviwo ndi amene ali ndi udindo wosamalira* chihema cha Umbonicho.”+
53 Alevi azimanga matenti awo mozungulira chihema cha Umboni kuti mkwiyo wa Mulungu usayakire Aisiraeli.+ Aleviwo ndi amene ali ndi udindo wosamalira* chihema cha Umbonicho.”+