Numeri 1:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Nthawi zonse mukamasamutsa chihema, Aleviwo azichipasula,+ ndipo mukafika pomanga msasa, Alevi ndi amene azimanga chihemacho. Munthu aliyense amene si Mlevi akayandikira chihemacho aziphedwa.+ Numeri 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Uike Aroni ndi ana ake kuti akhale ansembe, ndipo azigwira ntchito zawo zaunsembe.+ Munthu wamba* aliyense amene wayandikira malowo, aziphedwa.”+
51 Nthawi zonse mukamasamutsa chihema, Aleviwo azichipasula,+ ndipo mukafika pomanga msasa, Alevi ndi amene azimanga chihemacho. Munthu aliyense amene si Mlevi akayandikira chihemacho aziphedwa.+
10 Uike Aroni ndi ana ake kuti akhale ansembe, ndipo azigwira ntchito zawo zaunsembe.+ Munthu wamba* aliyense amene wayandikira malowo, aziphedwa.”+