Levitiko 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo zotsala pa nsembe yambewu zizikhala za Aroni ndi ana ake,+ chifukwa ndi zopatulika koposa,+ zochokera pansembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova.
3 Ndipo zotsala pa nsembe yambewu zizikhala za Aroni ndi ana ake,+ chifukwa ndi zopatulika koposa,+ zochokera pansembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova.