Levitiko 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Wansembe aziwotcha zinthu zonsezi paguwa lansembe monga chakudya.* Imeneyi ndi nsembe yowotcha pamoto yakafungo kosangalatsa.* Mafuta onse ndi a Yehova.+
16 Wansembe aziwotcha zinthu zonsezi paguwa lansembe monga chakudya.* Imeneyi ndi nsembe yowotcha pamoto yakafungo kosangalatsa.* Mafuta onse ndi a Yehova.+