Numeri 3:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Itanitsa fuko la Levi+ ndipo uwapereke kwa wansembe Aroni kuti azimutumikira.+ 7 Iwo azikwaniritsa udindo wawo pomuthandiza komanso potumikira gulu lonse pa ntchito zapachihema chokumanako. Numeri 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Iwe ndi ana ako, ndi nyumba yonse ya bambo ako, mudzayankha mlandu wa zolakwa zanu pa malamulo okhudza malo opatulika.+ Iweyo ndi ana ako mudzayankha mlandu wa zolakwa zanu pa malamulo okhudza unsembe wanu.+
6 “Itanitsa fuko la Levi+ ndipo uwapereke kwa wansembe Aroni kuti azimutumikira.+ 7 Iwo azikwaniritsa udindo wawo pomuthandiza komanso potumikira gulu lonse pa ntchito zapachihema chokumanako.
18 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Iwe ndi ana ako, ndi nyumba yonse ya bambo ako, mudzayankha mlandu wa zolakwa zanu pa malamulo okhudza malo opatulika.+ Iweyo ndi ana ako mudzayankha mlandu wa zolakwa zanu pa malamulo okhudza unsembe wanu.+