Oweruza 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anatumiza uthenga kwa mfumu ya Edomu+ wakuti: “Tiloleni tidutse nawo mʼdziko lanu,” koma mfumu ya Edomu inakana. Anatumizanso uthenga kwa mfumu ya Mowabu,+ koma nayonso sinalole. Choncho Aisiraeli anapitiriza kukhala ku Kadesi.+
17 Kenako anatumiza uthenga kwa mfumu ya Edomu+ wakuti: “Tiloleni tidutse nawo mʼdziko lanu,” koma mfumu ya Edomu inakana. Anatumizanso uthenga kwa mfumu ya Mowabu,+ koma nayonso sinalole. Choncho Aisiraeli anapitiriza kukhala ku Kadesi.+