Levitiko 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Nadabu ndi Abihu,+ omwe ndi ana a Aroni, aliyense anatenga chofukizira, nʼkuikamo moto ndi zofukiza+ pamwamba pake. Atatero anayamba kupereka zofukiza pamoto wosaloledwa+ ndi Yehova, umene iye sanawalamule. 1 Mbiri 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nadabu ndi Abihu anamwalira opanda ana aamuna bambo awo adakali ndi moyo,+ koma Eliezara+ ndi Itamara ankatumikirabe ngati ansembe.
10 Ndiyeno Nadabu ndi Abihu,+ omwe ndi ana a Aroni, aliyense anatenga chofukizira, nʼkuikamo moto ndi zofukiza+ pamwamba pake. Atatero anayamba kupereka zofukiza pamoto wosaloledwa+ ndi Yehova, umene iye sanawalamule.
2 Nadabu ndi Abihu anamwalira opanda ana aamuna bambo awo adakali ndi moyo,+ koma Eliezara+ ndi Itamara ankatumikirabe ngati ansembe.